Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 101 - طه - Page - Juz 16
﴿خَٰلِدِينَ فِيهِۖ وَسَآءَ لَهُمۡ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ حِمۡلٗا ﴾
[طه: 101]
﴿خالدين فيه وساء لهم يوم القيامة حملا﴾ [طه: 101]
Khaled Ibrahim Betala “Adzakhala m’menemo m’chilango. Ndipo ndi zoipa zedi (kwa anthu) kusenza mitolo (imeneyo) tsiku la Qiyâma |