Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 102 - طه - Page - Juz 16
﴿يَوۡمَ يُنفَخُ فِي ٱلصُّورِۚ وَنَحۡشُرُ ٱلۡمُجۡرِمِينَ يَوۡمَئِذٖ زُرۡقٗا ﴾
[طه: 102]
﴿يوم ينفخ في الصور ونحشر المجرمين يومئذ زرقا﴾ [طه: 102]
Khaled Ibrahim Betala “(Kumbuka Mtumiki Muhammad {s.a.w}), tsiku lomwe lipenga lidzaimbidwa. Ndipo tidzasonkhanitsa oipa tsiku limenelo maso awo ali a buluu (blue, chifukwa cha mantha) |