Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 18 - طه - Page - Juz 16
﴿قَالَ هِيَ عَصَايَ أَتَوَكَّؤُاْ عَلَيۡهَا وَأَهُشُّ بِهَا عَلَىٰ غَنَمِي وَلِيَ فِيهَا مَـَٔارِبُ أُخۡرَىٰ ﴾
[طه: 18]
﴿قال هي عصاي أتوكأ عليها وأهش بها على غنمي ولي فيها مآرب﴾ [طه: 18]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Iyi ndi ndodo yanga, ndimaitsamira (poyenda) ndi kuphopholera masamba a mbuzi zanga; ndiponso (m’ndodomo) muli zina zondithandiza.” |