×

Amene adakupangirani dziko lapansi kukhala ngati kama ndipo adakhazikitsa njira zoti inu 20:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ta-Ha ⮕ (20:53) ayat 53 in Chichewa

20:53 Surah Ta-Ha ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 53 - طه - Page - Juz 16

﴿ٱلَّذِي جَعَلَ لَكُمُ ٱلۡأَرۡضَ مَهۡدٗا وَسَلَكَ لَكُمۡ فِيهَا سُبُلٗا وَأَنزَلَ مِنَ ٱلسَّمَآءِ مَآءٗ فَأَخۡرَجۡنَا بِهِۦٓ أَزۡوَٰجٗا مِّن نَّبَاتٖ شَتَّىٰ ﴾
[طه: 53]

Amene adakupangirani dziko lapansi kukhala ngati kama ndipo adakhazikitsa njira zoti inu muziyendamo ndipo watumiza mvula kuchokera kumwamba. Ndipo ameretsa ndi iyo mitundu yosiyanasiyana ya mbewu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الذي جعل لكم الأرض مهدا وسلك لكم فيها سبلا وأنـزل من السماء, باللغة نيانجا

﴿الذي جعل لكم الأرض مهدا وسلك لكم فيها سبلا وأنـزل من السماء﴾ [طه: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Yemwe adakupangirani nthaka monga choyala, ndipo m’menemo adakuikirani njira ndikutsitsa madzi kuchokera kumwamba.” Ndipo kupyolera m’madziwo tidameretsa mmera wosiyanasiyana
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek