Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 52 - طه - Page - Juz 16
﴿قَالَ عِلۡمُهَا عِندَ رَبِّي فِي كِتَٰبٖۖ لَّا يَضِلُّ رَبِّي وَلَا يَنسَى ﴾
[طه: 52]
﴿قال علمها عند ربي في كتاب لا يضل ربي ولا ينسى﴾ [طه: 52]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Kudziwa kwa zimenezo nkwa Mbuye wanga, m’kaundula (Wake momwe mwasonkhanitsidwa chilichonse), Mbuye wanga sasokera, ndipo saiwala |