Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 60 - طه - Page - Juz 16
﴿فَتَوَلَّىٰ فِرۡعَوۡنُ فَجَمَعَ كَيۡدَهُۥ ثُمَّ أَتَىٰ ﴾
[طه: 60]
﴿فتولى فرعون فجمع كيده ثم أتى﴾ [طه: 60]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Farawo adabwerera ndikusonkhanitsa matsenga ake, ndipo kenako adabwera (ndi amatsenga ake pa tsiku la chipanganolo) |