Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 59 - طه - Page - Juz 16
﴿قَالَ مَوۡعِدُكُمۡ يَوۡمُ ٱلزِّينَةِ وَأَن يُحۡشَرَ ٱلنَّاسُ ضُحٗى ﴾
[طه: 59]
﴿قال موعدكم يوم الزينة وأن يحشر الناس ضحى﴾ [طه: 59]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Lonjezo lanu likhale pa tsiku lodzikongoletsa (tsiku la chikondwelero), ndipo anthu adzasonkhanitsidwe m’mawa.” |