×

Iwo adati, “Ife sitifuna iwe kuposa zizindikiro zimene zadza kwa ife ndi 20:72 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ta-Ha ⮕ (20:72) ayat 72 in Chichewa

20:72 Surah Ta-Ha ayat 72 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 72 - طه - Page - Juz 16

﴿قَالُواْ لَن نُّؤۡثِرَكَ عَلَىٰ مَا جَآءَنَا مِنَ ٱلۡبَيِّنَٰتِ وَٱلَّذِي فَطَرَنَاۖ فَٱقۡضِ مَآ أَنتَ قَاضٍۖ إِنَّمَا تَقۡضِي هَٰذِهِ ٱلۡحَيَوٰةَ ٱلدُّنۡيَآ ﴾
[طه: 72]

Iwo adati, “Ife sitifuna iwe kuposa zizindikiro zimene zadza kwa ife ndi Iye amene adatilenga ife. Kotero iwe chita chimene ufuna kuchita chifukwa iwe ukhoza kulamulira za m’moyo uno zokha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قالوا لن نؤثرك على ما جاءنا من البينات والذي فطرنا فاقض ما, باللغة نيانجا

﴿قالوا لن نؤثرك على ما جاءنا من البينات والذي فطرنا فاقض ما﴾ [طه: 72]

Khaled Ibrahim Betala
“(Amatsenga) adati: “Sitisankha iwe kusiya zomwe zatidzera; zisonyezo zachoonadi zoonekera poyera! Ndipo tikumlumbilira Yemwe adatilenga, (sitikusankha iwe), chita zomwe ufuna kuchita; ndithu iwe utha kupititsa chiweruzo chokhudzana ndi moyo uno wapansi, basi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek