Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 84 - طه - Page - Juz 16
﴿قَالَ هُمۡ أُوْلَآءِ عَلَىٰٓ أَثَرِي وَعَجِلۡتُ إِلَيۡكَ رَبِّ لِتَرۡضَىٰ ﴾
[طه: 84]
﴿قال هم أولاء على أثري وعجلت إليك رب لترضى﴾ [طه: 84]
Khaled Ibrahim Betala “Adati: “Iwo ali pambuyo panga akunditsata. Ndachita changu kudza kwa Inu, Mbuye wanga, kuti mundiyanje kwambiri.” |