Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 98 - طه - Page - Juz 16
﴿إِنَّمَآ إِلَٰهُكُمُ ٱللَّهُ ٱلَّذِي لَآ إِلَٰهَ إِلَّا هُوَۚ وَسِعَ كُلَّ شَيۡءٍ عِلۡمٗا ﴾
[طه: 98]
﴿إنما إلهكم الله الذي لا إله إلا هو وسع كل شيء علما﴾ [طه: 98]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu wompembedza wanu, ndi Allah Yekha, Yemwe, palibe woti nkupembedzedwa mwachoonadi koma Iye. Ndipo wakwanira pa chilichonse kuchidziwa ndi nzeru (Zake zopanda malire) |