Quran with Chichewa translation - Surah Ta-Ha ayat 99 - طه - Page - Juz 16
﴿كَذَٰلِكَ نَقُصُّ عَلَيۡكَ مِنۡ أَنۢبَآءِ مَا قَدۡ سَبَقَۚ وَقَدۡ ءَاتَيۡنَٰكَ مِن لَّدُنَّا ذِكۡرٗا ﴾
[طه: 99]
﴿كذلك نقص عليك من أنباء ما قد سبق وقد آتيناك من لدنا﴾ [طه: 99]
Khaled Ibrahim Betala “Umo ndi momwe tikukusimbira nkhani za (zinthu) zomwe zidatsogola (za aneneri). Ndithu takupatsa uthenga waukulu kuchokera kwa Ife (omwe ndi Qur’an) |