Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 111 - الأنبيَاء - Page - Juz 17
﴿وَإِنۡ أَدۡرِي لَعَلَّهُۥ فِتۡنَةٞ لَّكُمۡ وَمَتَٰعٌ إِلَىٰ حِينٖ ﴾ 
[الأنبيَاء: 111]
﴿وإن أدري لعله فتنة لكم ومتاع إلى حين﴾ [الأنبيَاء: 111]
| Khaled Ibrahim Betala ““Ndipo sindikudziwa, mwina kuchedwetsa chilango chanu ndi mayeso akukuyesani ndikukusangalatsani ndi zokoma (za m’dziko) mpaka Idzakwane nthawi yoikidwayo.” |