×

Iyayi! Ife timatumiza choonadi kuti chilimbane ndi bodza ndipo chimaliononga. Taonani, ilo 21:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:18) ayat 18 in Chichewa

21:18 Surah Al-Anbiya’ ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 18 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿بَلۡ نَقۡذِفُ بِٱلۡحَقِّ عَلَى ٱلۡبَٰطِلِ فَيَدۡمَغُهُۥ فَإِذَا هُوَ زَاهِقٞۚ وَلَكُمُ ٱلۡوَيۡلُ مِمَّا تَصِفُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 18]

Iyayi! Ife timatumiza choonadi kuti chilimbane ndi bodza ndipo chimaliononga. Taonani, ilo latha. Ndipo tsoka kwa inu chifukwa cha zimene mumanena

❮ Previous Next ❯

ترجمة: بل نقذف بالحق على الباطل فيدمغه فإذا هو زاهق ولكم الويل مما, باللغة نيانجا

﴿بل نقذف بالحق على الباطل فيدمغه فإذا هو زاهق ولكم الويل مما﴾ [الأنبيَاء: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Koma (chimene timachita ndi ichi), timachiponya choona pa chachabe ndi kuchiswa bongo bwake, ndipo chachabecho chimachoka. Ndipo chilango chili pa inu chifukwa cha zomwe mukunena (kumnamizira Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek