×

Ndipo Ife, iwe usadabwere sitidatumize ena, koma amuna omwe timawapatsa chivumbulutso. Motero 21:7 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:7) ayat 7 in Chichewa

21:7 Surah Al-Anbiya’ ayat 7 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 7 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿وَمَآ أَرۡسَلۡنَا قَبۡلَكَ إِلَّا رِجَالٗا نُّوحِيٓ إِلَيۡهِمۡۖ فَسۡـَٔلُوٓاْ أَهۡلَ ٱلذِّكۡرِ إِن كُنتُمۡ لَا تَعۡلَمُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 7]

Ndipo Ife, iwe usadabwere sitidatumize ena, koma amuna omwe timawapatsa chivumbulutso. Motero afunse anthu ozindikira ngati iwe siudziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما أرسلنا قبلك إلا رجالا نوحي إليهم فاسألوا أهل الذكر إن كنتم, باللغة نيانجا

﴿وما أرسلنا قبلك إلا رجالا نوحي إليهم فاسألوا أهل الذكر إن كنتم﴾ [الأنبيَاء: 7]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo sitidawatume patsogolo pako, (iwe Mtumiki,) koma anthu, (osati angelo); tidawavumbulutsira (chivumbulutso Chathu.) Choncho, afunseni eni kudziwa ngati inu simukudziwa (nkhani zakale)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek