Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 24 - الحج - Page - Juz 17
﴿وَهُدُوٓاْ إِلَى ٱلطَّيِّبِ مِنَ ٱلۡقَوۡلِ وَهُدُوٓاْ إِلَىٰ صِرَٰطِ ٱلۡحَمِيدِ ﴾
[الحج: 24]
﴿وهدوا إلى الطيب من القول وهدوا إلى صراط الحميد﴾ [الحج: 24]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adzatsogozedwa (kupita kumalo) kokamba mawu abwino okhaokha; ndiponso adzatsogozedwa ku njira ya Mwini kutamandidwa (kunjira yonkera ku Jannah) |