×

Zimenezo ndi chifukwa chakuti Mulungu ndiye choonadi ndipo Iye amapereka moyo ku 22:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:6) ayat 6 in Chichewa

22:6 Surah Al-hajj ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 6 - الحج - Page - Juz 17

﴿ذَٰلِكَ بِأَنَّ ٱللَّهَ هُوَ ٱلۡحَقُّ وَأَنَّهُۥ يُحۡيِ ٱلۡمَوۡتَىٰ وَأَنَّهُۥ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[الحج: 6]

Zimenezo ndi chifukwa chakuti Mulungu ndiye choonadi ndipo Iye amapereka moyo ku zinthu zakufa ndipo ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلك بأن الله هو الحق وأنه يحى الموتى وأنه على كل شيء, باللغة نيانجا

﴿ذلك بأن الله هو الحق وأنه يحى الموتى وأنه على كل شيء﴾ [الحج: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Zimenezo (monga kulenga munthu ndi kumeretsa mmera, ndi umboni wosonyeza) kuti Allah Woona alipo; ndikuti Iye amaukitsa akufa, ndiponso Iye ali ndi mphamvu pa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek