×

Ichi ndi chifukwa chakuti Mulungu amalowetsa usiku mu usana ndi kulowetsa usana 22:61 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:61) ayat 61 in Chichewa

22:61 Surah Al-hajj ayat 61 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 61 - الحج - Page - Juz 17

﴿ذَٰلِكَ بِأَنَّ ٱللَّهَ يُولِجُ ٱلَّيۡلَ فِي ٱلنَّهَارِ وَيُولِجُ ٱلنَّهَارَ فِي ٱلَّيۡلِ وَأَنَّ ٱللَّهَ سَمِيعُۢ بَصِيرٞ ﴾
[الحج: 61]

Ichi ndi chifukwa chakuti Mulungu amalowetsa usiku mu usana ndi kulowetsa usana mu usiku. Ndithudi Mulungu ndi wakumva ndi woona

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ذلك بأن الله يولج الليل في النهار ويولج النهار في الليل وأن, باللغة نيانجا

﴿ذلك بأن الله يولج الليل في النهار ويولج النهار في الليل وأن﴾ [الحج: 61]

Khaled Ibrahim Betala
“Zimenezo nchifukwa chakuti Allah amalowetsa usiku mu usana ndikulowetsa usana mu usiku, ndi chifukwanso chakuti ndithu Allah Ngwakumva Ngopenya
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek