Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 100 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿لَعَلِّيٓ أَعۡمَلُ صَٰلِحٗا فِيمَا تَرَكۡتُۚ كـَلَّآۚ إِنَّهَا كَلِمَةٌ هُوَ قَآئِلُهَاۖ وَمِن وَرَآئِهِم بَرۡزَخٌ إِلَىٰ يَوۡمِ يُبۡعَثُونَ ﴾
[المؤمنُون: 100]
﴿لعلي أعمل صالحا فيما تركت كلا إنها كلمة هو قائلها ومن ورائهم﴾ [المؤمنُون: 100]
Khaled Ibrahim Betala ““Kuti ndikachite zabwino pa zimene ndidasiya.” (Angelo amayankha kuti): “Iyayi! Ndithu awa ndi mawu basi amene iye akuyankhula (imfa ikamfika).” Ndipo patsogolo pawo pali chiyembekezo; (moyo wamasautso kwa oipa; ndipo wamtendere kwa abwino) kufikira tsiku limene adzaukitsidwa |