Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 1 - النور - Page - Juz 18
﴿سُورَةٌ أَنزَلۡنَٰهَا وَفَرَضۡنَٰهَا وَأَنزَلۡنَا فِيهَآ ءَايَٰتِۭ بَيِّنَٰتٖ لَّعَلَّكُمۡ تَذَكَّرُونَ ﴾
[النور: 1]
﴿سورة أنـزلناها وفرضناها وأنـزلنا فيها آيات بينات لعلكم تذكرون﴾ [النور: 1]
Khaled Ibrahim Betala “Iyi ndi Sura; taivumbulutsa, ndipo taikamo malamulo. Ndipo m’menemo tatumizamo Ayah (ndime) zomveka kuti mukumbukire (malamulo ndi kuchita nawo m’njira yoyenera) |