×

Iwo amanena monenetsa kuti, “Ife timakhulupirira mwa Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo 24:47 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:47) ayat 47 in Chichewa

24:47 Surah An-Nur ayat 47 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 47 - النور - Page - Juz 18

﴿وَيَقُولُونَ ءَامَنَّا بِٱللَّهِ وَبِٱلرَّسُولِ وَأَطَعۡنَا ثُمَّ يَتَوَلَّىٰ فَرِيقٞ مِّنۡهُم مِّنۢ بَعۡدِ ذَٰلِكَۚ وَمَآ أُوْلَٰٓئِكَ بِٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[النور: 47]

Iwo amanena monenetsa kuti, “Ife timakhulupirira mwa Mulungu ndi Mtumwi wake ndipo timawamvera onsewa.” Koma pambuyo pake ena a iwo amabwerera m’mbuyo. Ndithudi awa si okhulupirira ayi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويقولون آمنا بالله وبالرسول وأطعنا ثم يتولى فريق منهم من بعد ذلك, باللغة نيانجا

﴿ويقولون آمنا بالله وبالرسول وأطعنا ثم يتولى فريق منهم من بعد ذلك﴾ [النور: 47]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akunena (kuti): “Takhulupirira Allah ndi Mtumiki, ndipo tamvera.” Kenako ena a iwo amatembenuka pambuyo pa zimenezo; ndipo iwowo sali okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek