×

Ndithudi mwini wake wa chilichonse chimene chili kumwamba ndi dziko lapansi ndi 24:64 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:64) ayat 64 in Chichewa

24:64 Surah An-Nur ayat 64 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 64 - النور - Page - Juz 18

﴿أَلَآ إِنَّ لِلَّهِ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۖ قَدۡ يَعۡلَمُ مَآ أَنتُمۡ عَلَيۡهِ وَيَوۡمَ يُرۡجَعُونَ إِلَيۡهِ فَيُنَبِّئُهُم بِمَا عَمِلُواْۗ وَٱللَّهُ بِكُلِّ شَيۡءٍ عَلِيمُۢ ﴾
[النور: 64]

Ndithudi mwini wake wa chilichonse chimene chili kumwamba ndi dziko lapansi ndi Mulungu. Ndithudi Iye amadziwa zonse zimene zili m’mitima mwanu. Ndipo patsiku limene iwo adzabwerera kwa Iye, Iye adzawauza zonse zimene amachita. Ndipo Mulungu amadziwa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألا إن لله ما في السموات والأرض قد يعلم ما أنتم عليه, باللغة نيانجا

﴿ألا إن لله ما في السموات والأرض قد يعلم ما أنتم عليه﴾ [النور: 64]

Khaled Ibrahim Betala
“Mverani! Ndithu zili kumwamba ndi pansi nzake Allah, ndipo akudziwa zimene muli nazo. Ndipo patsiku limene adzabwezedwe kwa Iye, adzawauza zimene adachita ndipo Allah Ngodziwa chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek