×

“Mosakayika ndiwo amene adandisokoneza ine kuti ndisakhulupirire machenjezo a Mulungu pamene machenjezowo 25:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:29) ayat 29 in Chichewa

25:29 Surah Al-Furqan ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 29 - الفُرقَان - Page - Juz 19

﴿لَّقَدۡ أَضَلَّنِي عَنِ ٱلذِّكۡرِ بَعۡدَ إِذۡ جَآءَنِيۗ وَكَانَ ٱلشَّيۡطَٰنُ لِلۡإِنسَٰنِ خَذُولٗا ﴾
[الفُرقَان: 29]

“Mosakayika ndiwo amene adandisokoneza ine kuti ndisakhulupirire machenjezo a Mulungu pamene machenjezowo atandifika. Ndithudi Satana ndi wachinyengo nthawi zonse kwa munthu.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: لقد أضلني عن الذكر بعد إذ جاءني وكان الشيطان للإنسان خذولا, باللغة نيانجا

﴿لقد أضلني عن الذكر بعد إذ جاءني وكان الشيطان للإنسان خذولا﴾ [الفُرقَان: 29]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndithu adandisokeretsa kufikira ndidasiya ulaliki (wa Allah) utandidzera. Zoonadi, satana amataya munthu (akaona kuti wamgwetsa m’chionongeko).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek