Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 30 - الفُرقَان - Page - Juz 19
﴿وَقَالَ ٱلرَّسُولُ يَٰرَبِّ إِنَّ قَوۡمِي ٱتَّخَذُواْ هَٰذَا ٱلۡقُرۡءَانَ مَهۡجُورٗا ﴾
[الفُرقَان: 30]
﴿وقال الرسول يارب إن قومي اتخذوا هذا القرآن مهجورا﴾ [الفُرقَان: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Mtumiki (adasuma kwa Mbuye wake) adati: “E Mbuye wanga! Ndithu anthu anga aisandutsa Qur’aniyi kukhala chinthu chosiidwa, (sakuiwerenga. Ndiponso sakutsata ziphunzitso zake).” |