×

Komabe anthu osakhulupirira amapembedza milungu ina yoonjezera pa Mulungu weniweni imene siingathe 25:3 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:3) ayat 3 in Chichewa

25:3 Surah Al-Furqan ayat 3 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 3 - الفُرقَان - Page - Juz 18

﴿وَٱتَّخَذُواْ مِن دُونِهِۦٓ ءَالِهَةٗ لَّا يَخۡلُقُونَ شَيۡـٔٗا وَهُمۡ يُخۡلَقُونَ وَلَا يَمۡلِكُونَ لِأَنفُسِهِمۡ ضَرّٗا وَلَا نَفۡعٗا وَلَا يَمۡلِكُونَ مَوۡتٗا وَلَا حَيَوٰةٗ وَلَا نُشُورٗا ﴾
[الفُرقَان: 3]

Komabe anthu osakhulupirira amapembedza milungu ina yoonjezera pa Mulungu weniweni imene siingathe kulenga china chilichonse chifukwa chakuti nayonso idachita kulengedwa. Ndi imene singathe kuwathandiza kapena kuwaononga ndiponso imene ilibe mphamvu pa nkhani zokhudza imfa kapena moyo kapena kuukitsa anthu akufa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واتخذوا من دونه آلهة لا يخلقون شيئا وهم يخلقون ولا يملكون لأنفسهم, باللغة نيانجا

﴿واتخذوا من دونه آلهة لا يخلقون شيئا وهم يخلقون ولا يملكون لأنفسهم﴾ [الفُرقَان: 3]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek