×

Kodi wamuona iye amene amayesa zilakolako zake ngati milungu? Kodi iwe ungakhale 25:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:43) ayat 43 in Chichewa

25:43 Surah Al-Furqan ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 43 - الفُرقَان - Page - Juz 19

﴿أَرَءَيۡتَ مَنِ ٱتَّخَذَ إِلَٰهَهُۥ هَوَىٰهُ أَفَأَنتَ تَكُونُ عَلَيۡهِ وَكِيلًا ﴾
[الفُرقَان: 43]

Kodi wamuona iye amene amayesa zilakolako zake ngati milungu? Kodi iwe ungakhale munthu wosamalira munthu wotere

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أرأيت من اتخذ إلهه هواه أفأنت تكون عليه وكيلا, باللغة نيانجا

﴿أرأيت من اتخذ إلهه هواه أفأنت تكون عليه وكيلا﴾ [الفُرقَان: 43]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi wamuona yemwe wachichita chilakolako chake (chimene akuchikonda) kukhala mulungu wake? Kodi iweyo ungathe kukhala muyang’aniri wa iye (kotero kuti ungamkakamize chomwe safuna)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek