Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 56 - الفُرقَان - Page - Juz 19
﴿وَمَآ أَرۡسَلۡنَٰكَ إِلَّا مُبَشِّرٗا وَنَذِيرٗا ﴾ 
[الفُرقَان: 56]
﴿وما أرسلناك إلا مبشرا ونذيرا﴾ [الفُرقَان: 56]
| Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Ife sitidakutume koma kuti ukhale wouza nkhani zabwino (okhulupirira); ndi wochenjeza (osakhulupirira) |