×

Komabe anthu osakhulupirira amapembedza mafano moonjezerapa Mulungu Mafanowosangathekuwathandiza kapena kuwaononga. Munthu wosakhulupirira 25:55 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:55) ayat 55 in Chichewa

25:55 Surah Al-Furqan ayat 55 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 55 - الفُرقَان - Page - Juz 19

﴿وَيَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ مَا لَا يَنفَعُهُمۡ وَلَا يَضُرُّهُمۡۗ وَكَانَ ٱلۡكَافِرُ عَلَىٰ رَبِّهِۦ ظَهِيرٗا ﴾
[الفُرقَان: 55]

Komabe anthu osakhulupirira amapembedza mafano moonjezerapa Mulungu Mafanowosangathekuwathandiza kapena kuwaononga. Munthu wosakhulupirira amathandiza Satana kuchita zoipa zosakomera Ambuye wake

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويعبدون من دون الله ما لا ينفعهم ولا يضرهم وكان الكافر على, باللغة نيانجا

﴿ويعبدون من دون الله ما لا ينفعهم ولا يضرهم وكان الكافر على﴾ [الفُرقَان: 55]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (ena mwa anthu) akupembedza zina zake kusiya Allah, zomwe sizingawathandize ndiponso sizingawadzetsere masautso (atasiya kuzipembedza). Ndipo wosakhulupirira ndi mthandizi wa zoipa poukira Mbuye wake
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek