Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 119 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿فَأَنجَيۡنَٰهُ وَمَن مَّعَهُۥ فِي ٱلۡفُلۡكِ ٱلۡمَشۡحُونِ ﴾
[الشعراء: 119]
﴿فأنجيناه ومن معه في الفلك المشحون﴾ [الشعراء: 119]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho, tidampulumutsa pamodzi ndi omwe adali naye m’chombo chodzadza (ndi chilichonse chamoyo chomwe chidalipo m’dziko, chachimuna ndi chachikazi chidaikidwa m’menemo) |