Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 118 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿فَٱفۡتَحۡ بَيۡنِي وَبَيۡنَهُمۡ فَتۡحٗا وَنَجِّنِي وَمَن مَّعِيَ مِنَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ ﴾
[الشعراء: 118]
﴿فافتح بيني وبينهم فتحا ونجني ومن معي من المؤمنين﴾ [الشعراء: 118]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho weruzani pakati panga ndi pakati pa iwo (chiweruzo chabwino), ndipo ndipulumutseni pamodzi ndi amene alinane mwa okhulupirira.” |