Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 13 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿وَيَضِيقُ صَدۡرِي وَلَا يَنطَلِقُ لِسَانِي فَأَرۡسِلۡ إِلَىٰ هَٰرُونَ ﴾
[الشعراء: 13]
﴿ويضيق صدري ولا ينطلق لساني فأرسل إلى هارون﴾ [الشعراء: 13]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo chingabanike chifuwa changa (ndi maganizo, chifukwa chakunditsutsa kwawo); ndiponso lirime langa siliyankhula momveka bwino. Choncho tumizaninso uthengawu kwa Harun (kuti tikhale awiri ndipo azikandithangata pantchito yangayi) |