Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 14 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿وَلَهُمۡ عَلَيَّ ذَنۢبٞ فَأَخَافُ أَن يَقۡتُلُونِ ﴾
[الشعراء: 14]
﴿ولهم علي ذنب فأخاف أن يقتلون﴾ [الشعراء: 14]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo iwowo ndili nawo mlandu ndipo ndikuopa kuti angandiphe (pobwezera chimene ndidawalakwira powaphera munthu wawo) |