Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 155 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالَ هَٰذِهِۦ نَاقَةٞ لَّهَا شِرۡبٞ وَلَكُمۡ شِرۡبُ يَوۡمٖ مَّعۡلُومٖ ﴾
[الشعراء: 155]
﴿قال هذه ناقة لها شرب ولكم شرب يوم معلوم﴾ [الشعراء: 155]
Khaled Ibrahim Betala “Iye adati: “(Ndakubweretserani) ngamira iyi yaikazi; (koma) ili ndi gawo lake lakumwa, ndipo inu muli ndi gawo lanu lakutunga (madzi) patsiku lodziwika. (Tsiku lina lotunga rnadzi anthu).” |