Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 188 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالَ رَبِّيٓ أَعۡلَمُ بِمَا تَعۡمَلُونَ ﴾
[الشعراء: 188]
﴿قال ربي أعلم بما تعملون﴾ [الشعراء: 188]
Khaled Ibrahim Betala “(Shuaib) adati: “Mbuye wanga Ngodziwa kwambiri zimene mukuchita. (Akadzaona kuti inu ngoyenera kulangidwa ndizidutswa za thambo, adzakulangani).” |