Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 52 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿۞ وَأَوۡحَيۡنَآ إِلَىٰ مُوسَىٰٓ أَنۡ أَسۡرِ بِعِبَادِيٓ إِنَّكُم مُّتَّبَعُونَ ﴾
[الشعراء: 52]
﴿وأوحينا إلى موسى أن أسر بعبادي إنكم متبعون﴾ [الشعراء: 52]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo tidamvumbulutsira Mûsa (kuti): “Pita ndi anthu anga m’nthawi yausiku (musamuke m’dziko la Iguputo); ndithu inu mutsatidwa.” |