×

Winawamphamvu, amene adalimmodziwamajiniadati,“Inendidzakubweretseraniinu musadanyamuke pa mpando wanu. Ine ndili ndi mphamvu zonyamulira 27:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Naml ⮕ (27:39) ayat 39 in Chichewa

27:39 Surah An-Naml ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 39 - النَّمل - Page - Juz 19

﴿قَالَ عِفۡرِيتٞ مِّنَ ٱلۡجِنِّ أَنَا۠ ءَاتِيكَ بِهِۦ قَبۡلَ أَن تَقُومَ مِن مَّقَامِكَۖ وَإِنِّي عَلَيۡهِ لَقَوِيٌّ أَمِينٞ ﴾
[النَّمل: 39]

Winawamphamvu, amene adalimmodziwamajiniadati,“Inendidzakubweretseraniinu musadanyamuke pa mpando wanu. Ine ndili ndi mphamvu zonyamulira mpando ndiponso ndine wokhulupirika.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال عفريت من الجن أنا آتيك به قبل أن تقوم من مقامك, باللغة نيانجا

﴿قال عفريت من الجن أنا آتيك به قبل أن تقوم من مقامك﴾ [النَّمل: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Chiwanda chotchedwa Ifrit chidati: “Ine ndikubweletsera chimenecho usadaimilire pamalo ako (oweruzira). Ndipo ndithu ine pa icho (chimpando) ndine wanyonga, wokhulupirika.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek