×

Mpaka pamene adzafike pamalo a chiweruzo, Mulungu adzati, “Kodi inu mudakana chivumbulutso 27:84 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Naml ⮕ (27:84) ayat 84 in Chichewa

27:84 Surah An-Naml ayat 84 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 84 - النَّمل - Page - Juz 20

﴿حَتَّىٰٓ إِذَا جَآءُو قَالَ أَكَذَّبۡتُم بِـَٔايَٰتِي وَلَمۡ تُحِيطُواْ بِهَا عِلۡمًا أَمَّاذَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[النَّمل: 84]

Mpaka pamene adzafike pamalo a chiweruzo, Mulungu adzati, “Kodi inu mudakana chivumbulutso changa ngakhale kuti inu simumadziwa chilichonse cha chivumbulutsocho? Kodi ndi chiyani mumachita?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: حتى إذا جاءوا قال أكذبتم بآياتي ولم تحيطوا بها علما أماذا كنتم, باللغة نيانجا

﴿حتى إذا جاءوا قال أكذبتم بآياتي ولم تحيطوا بها علما أماذا كنتم﴾ [النَّمل: 84]

Khaled Ibrahim Betala
“Kufikira pomwe adzaza; (Allah) adzati: “Kodi inu mudazitsutsa Ayah (ndime) Zanga popanda kuzidziwa bwinobwino, nanga mumachita chiyani?”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek