×

Ndipo pamene iye adakula msinkhu ndi kukhala munthu wokwana, tidamupatsa iye luntha 28:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:14) ayat 14 in Chichewa

28:14 Surah Al-Qasas ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 14 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَلَمَّا بَلَغَ أَشُدَّهُۥ وَٱسۡتَوَىٰٓ ءَاتَيۡنَٰهُ حُكۡمٗا وَعِلۡمٗاۚ وَكَذَٰلِكَ نَجۡزِي ٱلۡمُحۡسِنِينَ ﴾
[القَصَص: 14]

Ndipo pamene iye adakula msinkhu ndi kukhala munthu wokwana, tidamupatsa iye luntha ndi nzeru. Mmenemu ndi mmene timalipirira anthu ochita zabwino

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولما بلغ أشده واستوى آتيناه حكما وعلما وكذلك نجزي المحسنين, باللغة نيانجا

﴿ولما بلغ أشده واستوى آتيناه حكما وعلما وكذلك نجزي المحسنين﴾ [القَصَص: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (Mûsa) pamene adakula nsinkhu wake ndi kulingana bwino tidampatsa nzeru ndi maphunziro. Ndipo umo ndimomwe timawalipirira ochita zabwino
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek