×

Ndipo ife tidaononga mibadwo yoyamba yakale ndipo tidamupatsa Mose Buku la Chipangano 28:43 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:43) ayat 43 in Chichewa

28:43 Surah Al-Qasas ayat 43 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 43 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَلَقَدۡ ءَاتَيۡنَا مُوسَى ٱلۡكِتَٰبَ مِنۢ بَعۡدِ مَآ أَهۡلَكۡنَا ٱلۡقُرُونَ ٱلۡأُولَىٰ بَصَآئِرَ لِلنَّاسِ وَهُدٗى وَرَحۡمَةٗ لَّعَلَّهُمۡ يَتَذَكَّرُونَ ﴾
[القَصَص: 43]

Ndipo ife tidaononga mibadwo yoyamba yakale ndipo tidamupatsa Mose Buku la Chipangano Chakale monga nyali, langizo ndi chifundo kwa anthu kuti mwina akhoza kuchenjezedwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد آتينا موسى الكتاب من بعد ما أهلكنا القرون الأولى بصائر للناس, باللغة نيانجا

﴿ولقد آتينا موسى الكتاب من بعد ما أهلكنا القرون الأولى بصائر للناس﴾ [القَصَص: 43]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu Mûsa tidampatsa buku pambuyo powononga mibadwo yoyamba kuti likhale chiphanulamaso cha anthu (kuti liwaunikire ku njira yolungama), ndi kuti likhale chiongoko ndi chifundo kuti iwo akumbukire
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek