×

Pamene limalakatulidwa kwa iwo, amati iwowo “Ife tili kulikhulupirira Bukuli chifukwa ndi 28:53 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:53) ayat 53 in Chichewa

28:53 Surah Al-Qasas ayat 53 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 53 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَإِذَا يُتۡلَىٰ عَلَيۡهِمۡ قَالُوٓاْ ءَامَنَّا بِهِۦٓ إِنَّهُ ٱلۡحَقُّ مِن رَّبِّنَآ إِنَّا كُنَّا مِن قَبۡلِهِۦ مُسۡلِمِينَ ﴾
[القَصَص: 53]

Pamene limalakatulidwa kwa iwo, amati iwowo “Ife tili kulikhulupirira Bukuli chifukwa ndi choonadi chochokera kwa Ambuye wathu. Ife tidadzipereka kwathunthu kalekale mawu awa asadadze.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا يتلى عليهم قالوا آمنا به إنه الحق من ربنا إنا كنا, باللغة نيانجا

﴿وإذا يتلى عليهم قالوا آمنا به إنه الحق من ربنا إنا كنا﴾ [القَصَص: 53]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo likawerengedwa kwa iwo, akuti: “Talikhulupirira; ndithu ichi nchoona chochokera kwa Mbuye wathu; ndithu ilo lisanadze ife tidali Asilamu (ogonjera Allah).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek