×

Ndikuwakhazikitsa m’dziko ndipo tinamupatsa Farawo, Hamani ndi gulu lawo la nkhondo zimene 28:6 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:6) ayat 6 in Chichewa

28:6 Surah Al-Qasas ayat 6 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 6 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَنُمَكِّنَ لَهُمۡ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَنُرِيَ فِرۡعَوۡنَ وَهَٰمَٰنَ وَجُنُودَهُمَا مِنۡهُم مَّا كَانُواْ يَحۡذَرُونَ ﴾
[القَصَص: 6]

Ndikuwakhazikitsa m’dziko ndipo tinamupatsa Farawo, Hamani ndi gulu lawo la nkhondo zimene iwo anali kuopa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ونمكن لهم في الأرض ونري فرعون وهامان وجنودهما منهم ما كانوا يحذرون, باللغة نيانجا

﴿ونمكن لهم في الأرض ونري فرعون وهامان وجنودهما منهم ما كانوا يحذرون﴾ [القَصَص: 6]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi kuwapatsa mphamvu za pa dziko (kuti azichita mmene angafunire) ndi kuti timuonetse Farawo ndi Hamana ndi magulu awo ankhondo kuchokera kwa iwo (ana a Israel), zomwe amaziwopa (kuti zingawathetsere ufumu wawo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek