×

Koma chidali chifuniro chathu kuti tiwapatse zabwino anthu amene adali oponderezedwa pa 28:5 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:5) ayat 5 in Chichewa

28:5 Surah Al-Qasas ayat 5 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 5 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَنُرِيدُ أَن نَّمُنَّ عَلَى ٱلَّذِينَ ٱسۡتُضۡعِفُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَنَجۡعَلَهُمۡ أَئِمَّةٗ وَنَجۡعَلَهُمُ ٱلۡوَٰرِثِينَ ﴾
[القَصَص: 5]

Koma chidali chifuniro chathu kuti tiwapatse zabwino anthu amene adali oponderezedwa pa dziko ndi kuwasandutsa iwo kukhala atsogoleri a anthu ndi kuwapanga iwo kulowa m’malo mwa ufumu wa Farawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ونريد أن نمن على الذين استضعفوا في الأرض ونجعلهم أئمة ونجعلهم الوارثين, باللغة نيانجا

﴿ونريد أن نمن على الذين استضعفوا في الأرض ونجعلهم أئمة ونجعلهم الوارثين﴾ [القَصَص: 5]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidafuna kuwachitira zabwino amene adafooketsedwa m’dziko (la Iguputo), ndi kuwachita kukhala atsogoleri ndi kuwachitanso kukhala amlowa mmalo ( a Baiti Al-Makadasi)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek