×

Iwo amene adzapezeka ndi mlandu wotere adzati, “Awa ndiwo anthu amene ife 28:63 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:63) ayat 63 in Chichewa

28:63 Surah Al-Qasas ayat 63 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 63 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿قَالَ ٱلَّذِينَ حَقَّ عَلَيۡهِمُ ٱلۡقَوۡلُ رَبَّنَا هَٰٓؤُلَآءِ ٱلَّذِينَ أَغۡوَيۡنَآ أَغۡوَيۡنَٰهُمۡ كَمَا غَوَيۡنَاۖ تَبَرَّأۡنَآ إِلَيۡكَۖ مَا كَانُوٓاْ إِيَّانَا يَعۡبُدُونَ ﴾
[القَصَص: 63]

Iwo amene adzapezeka ndi mlandu wotere adzati, “Awa ndiwo anthu amene ife tidawasocheretsa. Ife tidawasocheretsa chifukwa nafenso tidali osochera. Ife tsopano tadzipatula (kuchoka mwa iwo) ndi kudza kwa inu. Si ndife amene iwo anali kupembedza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال الذين حق عليهم القول ربنا هؤلاء الذين أغوينا أغويناهم كما غوينا, باللغة نيانجا

﴿قال الذين حق عليهم القول ربنا هؤلاء الذين أغوينا أغويناهم كما غوينا﴾ [القَصَص: 63]

Khaled Ibrahim Betala
“Adzanena amene mawu (onena za chilango) atsimikizika pa iwo: “Mbuye wathu! Awa ndiamene tidawasokeretsa; tidawasokeretsa monga momwe Tidasokelera. tikudzipatula ndi iwo kwa inu; samatilambira ife.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek