×

Ndithudi Karuni, mosakayika, adali wa ku mtundu wa Mose. Koma iye amawanyoza 28:76 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:76) ayat 76 in Chichewa

28:76 Surah Al-Qasas ayat 76 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 76 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿۞ إِنَّ قَٰرُونَ كَانَ مِن قَوۡمِ مُوسَىٰ فَبَغَىٰ عَلَيۡهِمۡۖ وَءَاتَيۡنَٰهُ مِنَ ٱلۡكُنُوزِ مَآ إِنَّ مَفَاتِحَهُۥ لَتَنُوٓأُ بِٱلۡعُصۡبَةِ أُوْلِي ٱلۡقُوَّةِ إِذۡ قَالَ لَهُۥ قَوۡمُهُۥ لَا تَفۡرَحۡۖ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يُحِبُّ ٱلۡفَرِحِينَ ﴾
[القَصَص: 76]

Ndithudi Karuni, mosakayika, adali wa ku mtundu wa Mose. Koma iye amawanyoza iwo chifukwa Ife tidamupatsa nkhokwe za chuma zimene ndithudi makiyi ake samatheka kunyamulidwa ndi anthu angapo a mphamvu. Anthu ake adati kwa iye, “Usadzikundikire chifukwa Mulungu sakonda anthu odzikundikira chifukwa cha chuma.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن قارون كان من قوم موسى فبغى عليهم وآتيناه من الكنوز ما, باللغة نيانجا

﴿إن قارون كان من قوم موسى فبغى عليهم وآتيناه من الكنوز ما﴾ [القَصَص: 76]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Qaruni adali mwa anthu a Mûsa; koma adazikweza kwa iwo, ndipo tidampatsa nkhokwe za chuma zomwe makiyi ake ngolemetsa kagulu ka anthu anyonga (kuwasenza). Anthu ake adamuuza: “Usanyade; ndithu Allah sakonda onyada.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek