×

“Koma ufunefune, kudzera m’zimene Mulungu wakupatsa iwe, kuti upeze moyo umene uli 28:77 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:77) ayat 77 in Chichewa

28:77 Surah Al-Qasas ayat 77 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 77 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَٱبۡتَغِ فِيمَآ ءَاتَىٰكَ ٱللَّهُ ٱلدَّارَ ٱلۡأٓخِرَةَۖ وَلَا تَنسَ نَصِيبَكَ مِنَ ٱلدُّنۡيَاۖ وَأَحۡسِن كَمَآ أَحۡسَنَ ٱللَّهُ إِلَيۡكَۖ وَلَا تَبۡغِ ٱلۡفَسَادَ فِي ٱلۡأَرۡضِۖ إِنَّ ٱللَّهَ لَا يُحِبُّ ٱلۡمُفۡسِدِينَ ﴾
[القَصَص: 77]

“Koma ufunefune, kudzera m’zimene Mulungu wakupatsa iwe, kuti upeze moyo umene uli nkudza, ndiponso usaiwale udindo wako m’dziko lino. Khala wabwino monga Mulungu wakuonetsera ubwino wake. Ndipo usalimbike pochita zoipa padziko lapansi chifukwa Mulungu sakonda anthu ochita zoipa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وابتغ فيما آتاك الله الدار الآخرة ولا تنس نصيبك من الدنيا وأحسن, باللغة نيانجا

﴿وابتغ فيما آتاك الله الدار الآخرة ولا تنس نصيبك من الدنيا وأحسن﴾ [القَصَص: 77]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndipo uyifunefune kupyolera m’zomwe Allah wakupatsa, nyumba yabwino yomaliza, usaiwale gawo lako la m’dziko; chita zabwino monga momwe Allah wakuchitira zabwino, ndipo usafune kuononga pa dziko; ndithu Allah sakonda oononga.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek