Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 87 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿وَلَا يَصُدُّنَّكَ عَنۡ ءَايَٰتِ ٱللَّهِ بَعۡدَ إِذۡ أُنزِلَتۡ إِلَيۡكَۖ وَٱدۡعُ إِلَىٰ رَبِّكَۖ وَلَا تَكُونَنَّ مِنَ ٱلۡمُشۡرِكِينَ ﴾
[القَصَص: 87]
﴿ولا يصدنك عن آيات الله بعد إذ أنـزلت إليك وادع إلى ربك﴾ [القَصَص: 87]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo asakutsekereze kutsatira ndime za (mawu a) Allah pa mbuyo povumbulutsidwa pa iwe, ndipo aitanire anthu kwa Mbuye wako, komatu usakhale m’gulu la anthu omphatikiza Allah ndi mafano |