Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 86 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿وَمَا كُنتَ تَرۡجُوٓاْ أَن يُلۡقَىٰٓ إِلَيۡكَ ٱلۡكِتَٰبُ إِلَّا رَحۡمَةٗ مِّن رَّبِّكَۖ فَلَا تَكُونَنَّ ظَهِيرٗا لِّلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[القَصَص: 86]
﴿وما كنت ترجو أن يلقى إليك الكتاب إلا رحمة من ربك فلا﴾ [القَصَص: 86]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo iwe sudali kulakalaka kuti ungapatsidwe buku (pamodzi ndi uneneri) koma izi zidachitika pa chifundo chochokera kwa Mbuye wako; choncho usakhale m’thandizi wa anthu osakhulupirira (Allah) |