×

Ndipo pakati pa anthu pali iye amene amati, “Ife timakhulupirira mwa Mulungu.” 29:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:10) ayat 10 in Chichewa

29:10 Surah Al-‘Ankabut ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 10 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَمِنَ ٱلنَّاسِ مَن يَقُولُ ءَامَنَّا بِٱللَّهِ فَإِذَآ أُوذِيَ فِي ٱللَّهِ جَعَلَ فِتۡنَةَ ٱلنَّاسِ كَعَذَابِ ٱللَّهِۖ وَلَئِن جَآءَ نَصۡرٞ مِّن رَّبِّكَ لَيَقُولُنَّ إِنَّا كُنَّا مَعَكُمۡۚ أَوَلَيۡسَ ٱللَّهُ بِأَعۡلَمَ بِمَا فِي صُدُورِ ٱلۡعَٰلَمِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 10]

Ndipo pakati pa anthu pali iye amene amati, “Ife timakhulupirira mwa Mulungu.” Koma akangoona mavuto chifukwa chodzipereka kwa Mulungu, amaganiza kuti kuponderezedwa kwawo ndi anthu ndi mkwiyo wochokera kwa Mulungu! Ndipo ngati thandizo lidza kwa iwe kuchokera kwa Ambuye wako, ndithudi, iwo adzati, “Ife tidali kumbali yako.” Kodi mukuganiza kuti Mulungu sadziwa zonse zimene zili m’mitima mwawo pakati pa zolengedwa zake zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن الناس من يقول آمنا بالله فإذا أوذي في الله جعل فتنة, باللغة نيانجا

﴿ومن الناس من يقول آمنا بالله فإذا أوذي في الله جعل فتنة﴾ [العَنكبُوت: 10]

❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek