×

Ndipo iye adati, “Inu mwasankha kupembedza mafano kuonjezera pa Mulungu weniweni chifukwa 29:25 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:25) ayat 25 in Chichewa

29:25 Surah Al-‘Ankabut ayat 25 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 25 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَقَالَ إِنَّمَا ٱتَّخَذۡتُم مِّن دُونِ ٱللَّهِ أَوۡثَٰنٗا مَّوَدَّةَ بَيۡنِكُمۡ فِي ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَاۖ ثُمَّ يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِ يَكۡفُرُ بَعۡضُكُم بِبَعۡضٖ وَيَلۡعَنُ بَعۡضُكُم بَعۡضٗا وَمَأۡوَىٰكُمُ ٱلنَّارُ وَمَا لَكُم مِّن نَّٰصِرِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 25]

Ndipo iye adati, “Inu mwasankha kupembedza mafano kuonjezera pa Mulungu weniweni chifukwa chokweza mgwirizano wa pakati panu m’moyo uno. Koma pa tsiku lachiweruzo inu mudzakanana wina ndi mnzake. Ndipo malo anu akakhala ku moto ndipo inu simudzakhala ndi wina wokuthandizani.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال إنما اتخذتم من دون الله أوثانا مودة بينكم في الحياة الدنيا, باللغة نيانجا

﴿وقال إنما اتخذتم من دون الله أوثانا مودة بينكم في الحياة الدنيا﴾ [العَنكبُوت: 25]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adanena: “Ndithu inu mwasankha mafano kukhala milungu kusiya Allah, ndipo mukukondana pakati panu m’moyo wa pa dziko; (pokhalirana pamodzi ndi kupitiriza kupembedza mafanowo mwachimvano). Koma tsiku la Qiyâma, mudzakanana wina ndi mnzake, komanso mudzatembelerana wina ndi mnzake, malo anu adzakhala ku Moto, ndipo simudzapeza okupulumutsani.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek