×

Yankho la anthu a Abrahamu lidali lamwano ndipo adati, “Mumuphe kapena mumutenthe.” 29:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:24) ayat 24 in Chichewa

29:24 Surah Al-‘Ankabut ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 24 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿فَمَا كَانَ جَوَابَ قَوۡمِهِۦٓ إِلَّآ أَن قَالُواْ ٱقۡتُلُوهُ أَوۡ حَرِّقُوهُ فَأَنجَىٰهُ ٱللَّهُ مِنَ ٱلنَّارِۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٖ لِّقَوۡمٖ يُؤۡمِنُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 24]

Yankho la anthu a Abrahamu lidali lamwano ndipo adati, “Mumuphe kapena mumutenthe.” Koma Mulungu adamupulumutsa iye ku moto. Ndithudi mu zimenezi muli phunziro kwa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فما كان جواب قومه إلا أن قالوا اقتلوه أو حرقوه فأنجاه الله, باللغة نيانجا

﴿فما كان جواب قومه إلا أن قالوا اقتلوه أو حرقوه فأنجاه الله﴾ [العَنكبُوت: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho yankho la anthu ake silidali lina koma adangoti: “Mupheni kapena mtentheni ndi moto.” Koma Allah adampulumutsa ku moto. Ndithu m’zimenezi muli zisonyezo (zosonyeza mphamvu za Allah) kwa anthu okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek