×

Koma Loti adamukhulupirira iye. Iye adati, “Ndidzachoka pa nyumba yanga chifukwa cha 29:26 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:26) ayat 26 in Chichewa

29:26 Surah Al-‘Ankabut ayat 26 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 26 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿۞ فَـَٔامَنَ لَهُۥ لُوطٞۘ وَقَالَ إِنِّي مُهَاجِرٌ إِلَىٰ رَبِّيٓۖ إِنَّهُۥ هُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[العَنكبُوت: 26]

Koma Loti adamukhulupirira iye. Iye adati, “Ndidzachoka pa nyumba yanga chifukwa cha Ambuye wanga chifukwa Iye ndi wamphamvu zambiri ndi wanzeru.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فآمن له لوط وقال إني مهاجر إلى ربي إنه هو العزيز الحكيم, باللغة نيانجا

﴿فآمن له لوط وقال إني مهاجر إلى ربي إنه هو العزيز الحكيم﴾ [العَنكبُوت: 26]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho (Mneneri) Luti adamkhulupirira iye. Ndipo (Mneneri Ibrahim) adanena: “Ndithu ine ndikusamukira kwa Mbuye wanga (ku dziko lomwe wandilamulira). Ndithu Iye Ngwamphamvu zoposa Ngwanzeru zakuya.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek